Salimo 74:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 74 Inu Mulungu, n’chifukwa chiyani mwatitaya?+N’chifukwa chiyani mkwiyo wanu ukuyakira nkhosa zimene mukuweta?+ Salimo 79:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Haa! Inu Yehova, mukhala wokwiya mpaka liti? Kwamuyaya?+Kodi mkwiyo wanu udzakhala ukuyaka ngati moto mpaka liti?+
74 Inu Mulungu, n’chifukwa chiyani mwatitaya?+N’chifukwa chiyani mkwiyo wanu ukuyakira nkhosa zimene mukuweta?+
5 Haa! Inu Yehova, mukhala wokwiya mpaka liti? Kwamuyaya?+Kodi mkwiyo wanu udzakhala ukuyaka ngati moto mpaka liti?+