7 M’malo mwa manyazi, mudzalandira zinthu zochuluka kuwirikiza kawiri,+ ndipo m’malo mochita manyazi, anthu anga adzafuula ndi chisangalalo chifukwa cha gawo lawo.+ Iwo adzakhala ndi gawo lowirikiza kawiri m’dziko lawo,+ ndipo adzasangalala mpaka kalekale.+