1 Samueli 30:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Chotero mwamunayo anaperekeza+ Davide ndi kupita kumene kunali achifwambawo, ndipo anawapeza atamwazikana m’dziko lonselo, akudya ndi kumwa, kuchita chiphwando+ chifukwa chakuti anafunkha zinthu zambiri m’dziko la Afilisiti ndi la Yuda.+ 2 Mbiri 20:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Kenako Ayuda ndi anthu onse a ku Yerusalemu anabwerera ku Yerusalemu, Yehosafati ali patsogolo pawo. Iwo anali akusangalala chifukwa Yehova anawathandiza kugonjetsa adani awo.+
16 Chotero mwamunayo anaperekeza+ Davide ndi kupita kumene kunali achifwambawo, ndipo anawapeza atamwazikana m’dziko lonselo, akudya ndi kumwa, kuchita chiphwando+ chifukwa chakuti anafunkha zinthu zambiri m’dziko la Afilisiti ndi la Yuda.+
27 Kenako Ayuda ndi anthu onse a ku Yerusalemu anabwerera ku Yerusalemu, Yehosafati ali patsogolo pawo. Iwo anali akusangalala chifukwa Yehova anawathandiza kugonjetsa adani awo.+