1 Akorinto 15:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pakuti monga mwa Adamu onse akufa,+ momwemonso mwa Khristu onse adzapatsidwa+ moyo. Aheberi 9:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choncho iye analowa m’malo oyera amkatikati ndi magazi+ ake, osati ndi magazi a mbuzi kapena a ng’ombe zazing’ono zamphongo. Analowa kamodzi kokha m’malo oyera amkatikatiwo, ndipo anatilanditsa kwamuyaya.+ Chivumbulutso 1:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 ndiponso wamoyo.+ Ndinali wakufa,+ koma taona, ndili ndi moyo kwamuyaya,+ ndipo ndili ndi makiyi a imfa+ ndi a Manda.*+
12 Choncho iye analowa m’malo oyera amkatikati ndi magazi+ ake, osati ndi magazi a mbuzi kapena a ng’ombe zazing’ono zamphongo. Analowa kamodzi kokha m’malo oyera amkatikatiwo, ndipo anatilanditsa kwamuyaya.+
18 ndiponso wamoyo.+ Ndinali wakufa,+ koma taona, ndili ndi moyo kwamuyaya,+ ndipo ndili ndi makiyi a imfa+ ndi a Manda.*+