Salimo 45:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mulungu ndiye mpando wako wachifumu mpaka kalekale, ndithu mpaka muyaya.+Ndodo yako yachifumu ndiyo ndodo yachilungamo.+ Yesaya 16:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Mpando wachifumu ndithu udzakhazikika ndi kukoma mtima kosatha.+ Mfumu idzakhala pampandowo n’kumalamulira mokhulupirika muhema wa Davide.+ Izidzaweruza n’kumafunafuna chilungamo, ndipo izidzachita mwachangu zinthu zoyenera.”+ Yesaya 32:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Taonani! Mfumu+ idzalamulira mwachilungamo,+ ndipo akalonga+ adzalamuliranso mwachilungamo. Yohane 5:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ine sindingachite chilichonse chongoganiza ndekha. Ndimaweruza malinga ndi mmene ndamvera, ndipo chiweruzo chimene ndimapereka n’cholungama,+ chifukwa sinditsatira chifuniro changa, koma chifuniro+ cha amene anandituma. Aheberi 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma ponena za Mwana wake, iye akuti: “Mulungu ndiye mpando wako wachifumu mpaka muyaya,+ ndipo ndodo ya ufumu+ wako ndiyo ndodo yachilungamo.+
6 Mulungu ndiye mpando wako wachifumu mpaka kalekale, ndithu mpaka muyaya.+Ndodo yako yachifumu ndiyo ndodo yachilungamo.+
5 “Mpando wachifumu ndithu udzakhazikika ndi kukoma mtima kosatha.+ Mfumu idzakhala pampandowo n’kumalamulira mokhulupirika muhema wa Davide.+ Izidzaweruza n’kumafunafuna chilungamo, ndipo izidzachita mwachangu zinthu zoyenera.”+
30 Ine sindingachite chilichonse chongoganiza ndekha. Ndimaweruza malinga ndi mmene ndamvera, ndipo chiweruzo chimene ndimapereka n’cholungama,+ chifukwa sinditsatira chifuniro changa, koma chifuniro+ cha amene anandituma.
8 Koma ponena za Mwana wake, iye akuti: “Mulungu ndiye mpando wako wachifumu mpaka muyaya,+ ndipo ndodo ya ufumu+ wako ndiyo ndodo yachilungamo.+