Yesaya 47:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iwe mwana wamkazi wa Akasidi,+ khala pansi mwakachetechete+ ndipo ulowe mu mdima.+ Pakuti anthu sadzakutchulanso kuti Dona+ wa Maufumu.+ Yeremiya 51:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Iwe mkazi wokhala pamadzi ambiri,+ wokhala ndi chuma chochuluka,+ mapeto ako afika ndipo nthawi yako+ yoti uzipanga phindu yatha.+ Danieli 4:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Mfumuyo inali kunena kuti:+ “Kodi uyu si Babulo Wamkulu amene ine ndamanga ndi mphamvu zanga zazikulu+ ndiponso ndi ulemerero wanga waukulu ndi cholinga chakuti kukhale nyumba yachifumu?”+
5 Iwe mwana wamkazi wa Akasidi,+ khala pansi mwakachetechete+ ndipo ulowe mu mdima.+ Pakuti anthu sadzakutchulanso kuti Dona+ wa Maufumu.+
13 “Iwe mkazi wokhala pamadzi ambiri,+ wokhala ndi chuma chochuluka,+ mapeto ako afika ndipo nthawi yako+ yoti uzipanga phindu yatha.+
30 Mfumuyo inali kunena kuti:+ “Kodi uyu si Babulo Wamkulu amene ine ndamanga ndi mphamvu zanga zazikulu+ ndiponso ndi ulemerero wanga waukulu ndi cholinga chakuti kukhale nyumba yachifumu?”+