Deuteronomo 28:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Udzalonjeza kukwatira mkazi koma mwamuna wina adzamugwirira.+ Udzamanga nyumba koma sudzakhalamo.+ Udzabzala mitengo ya mpesa koma sudzadya zipatso zake.+ Yeremiya 12:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Afesa tirigu koma akolola minga.+ Agwira ntchito mpaka kudwala nayo, koma osapeza phindu lililonse.+ Iwo adzachita manyazi ndi zokolola zawo chifukwa mkwiyo waukulu wa Yehova udzawayakira.” Hoseya 8:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Iwo akungofesa mphepo, ndipo adzakolola mphepo yamkuntho.+ Tirigu amene ali m’minda yawo sakukula.+ Mbewu zawo sizikuwapatsa ufa.+ Ngati zina mwa mbewuzo zingabereke, alendo adzazimeza.+ Zefaniya 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Chuma chawo chidzafunkhidwa ndipo nyumba zawo zidzakhala bwinja.+ Iwo adzamanga nyumba, koma sadzakhalamo.+ Iwo adzalima minda ya mpesa koma sadzamwa vinyo wochokera mmenemo.+
30 Udzalonjeza kukwatira mkazi koma mwamuna wina adzamugwirira.+ Udzamanga nyumba koma sudzakhalamo.+ Udzabzala mitengo ya mpesa koma sudzadya zipatso zake.+
13 Afesa tirigu koma akolola minga.+ Agwira ntchito mpaka kudwala nayo, koma osapeza phindu lililonse.+ Iwo adzachita manyazi ndi zokolola zawo chifukwa mkwiyo waukulu wa Yehova udzawayakira.”
7 “Iwo akungofesa mphepo, ndipo adzakolola mphepo yamkuntho.+ Tirigu amene ali m’minda yawo sakukula.+ Mbewu zawo sizikuwapatsa ufa.+ Ngati zina mwa mbewuzo zingabereke, alendo adzazimeza.+
13 Chuma chawo chidzafunkhidwa ndipo nyumba zawo zidzakhala bwinja.+ Iwo adzamanga nyumba, koma sadzakhalamo.+ Iwo adzalima minda ya mpesa koma sadzamwa vinyo wochokera mmenemo.+