Yesaya 62:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 62 Chifukwa cha Ziyoni sindidzakhala phee,+ ndipo chifukwa cha Yerusalemu+ sindidzakhala chete mpaka kulungama kwake kutakhala ngati kuwala,+ ndiponso mpaka chipulumutso chake chitakhala ngati muuni woyaka moto.+ Zekariya 8:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndithu ndidzawabweretsa, ndipo adzakhala mu Yerusalemu.+ Iwo adzakhala anthu anga+ ndipo ine ndidzakhala Mulungu wawo woona ndi wachilungamo.’”+
62 Chifukwa cha Ziyoni sindidzakhala phee,+ ndipo chifukwa cha Yerusalemu+ sindidzakhala chete mpaka kulungama kwake kutakhala ngati kuwala,+ ndiponso mpaka chipulumutso chake chitakhala ngati muuni woyaka moto.+
8 Ndithu ndidzawabweretsa, ndipo adzakhala mu Yerusalemu.+ Iwo adzakhala anthu anga+ ndipo ine ndidzakhala Mulungu wawo woona ndi wachilungamo.’”+