4 Mesa+ mfumu ya Mowabu anali woweta nkhosa. Ankapereka kwa mfumu ya Isiraeli ana a nkhosa 100,000, ndi nkhosa zamphongo zosameta ubweya zokwana 100,000 monga msonkho.
8 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Popeza kuti Mowabu+ ndi Seiri+ anena kuti: “Taonani! Nyumba ya Yuda ili ngati mitundu ina yonse ya anthu,”+