29 “Tamva za kunyada kwa Mowabu.+ Iye ndi wodzikuza kwambiri. Tamva za kudzikweza kwake, kunyada kwake, kudzikuza kwake ndi kudzitukumula kwa mtima wake.”+
8 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Popeza kuti Mowabu+ ndi Seiri+ anena kuti: “Taonani! Nyumba ya Yuda ili ngati mitundu ina yonse ya anthu,”+
8 “Ndamva chitonzo cha Mowabu+ ndi mawu onyoza a ana a Amoni+ amene anali kunena kwa anthu anga. Iwo anali kuopseza anthu anga modzitukumula kuti awalanda dziko lawo.”