21 Ponena za Ahabu mwana wa Kolaya ndi Zedekiya mwana wa Maaseya amene akulosera m’dzina langa monama pakati panu,+ Yehova wa makamu, Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Anthu amenewa ndikuwapereka m’manja mwa Nebukadirezara mfumu ya Babulo, ndipo adzawapha inu mukuona.+