Yesaya 1:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndidzakubweretseraninso oweruza ngati pa chiyambi paja, ndi aphungu ngati poyamba paja.+ Pambuyo pa zimenezi mudzatchedwa Mzinda Wachilungamo ndi Mzinda Wokhulupirika.+
26 Ndidzakubweretseraninso oweruza ngati pa chiyambi paja, ndi aphungu ngati poyamba paja.+ Pambuyo pa zimenezi mudzatchedwa Mzinda Wachilungamo ndi Mzinda Wokhulupirika.+