Miyambo 1:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Popeza ndaitana koma inu mukupitiriza kukana,+ ndatambasula dzanja langa koma palibe amene akumvetsera,+ Yesaya 65:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choncho ine ndidzakonzeratu zoti anthu inu mudzaphedwe ndi lupanga.+ Nonsenu mudzawerama kuti akupheni,+ popeza ndinakuitanani+ koma simunayankhe. Ndinalankhula koma simunamvere.+ Munapitiriza kuchita zinthu zoipa pamaso panga+ ndipo munasankha zinthu zimene sindisangalala nazo.”+ Yesaya 66:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ineyo ndidzasankha njira zowazunzira.+ Ndidzawabweretsera zinthu zimene amachita nazo mantha+ chifukwa ndinaitana koma palibe amene anayankha. Ndinalankhula koma palibe amene anamvera.+ Iwo anapitiriza kuchita zinthu zoipa pamaso panga ndipo anasankha zinthu zimene sindisangalala nazo.”+ Yeremiya 7:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tsopano chifukwa chakuti mwapitiriza kuchita ntchito zimenezi,’ watero Yehova, ‘ndipo ndinali kukulankhulani nthawi zonse, kudzuka m’mamawa ndi kukulankhulani,+ koma inu osamva,+ kukuitanani koma inu osandiyankha,+ Yeremiya 26:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 komanso kumvera mawu a atumiki anga aneneri amene ndikuwatumiza kwa inu, kudzuka m’mawa kwambiri ndi kuwatumiza, amene inu simunawamvere,+ Yeremiya 32:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Iwo anali kundifulatira, sanandiyang’ane.+ Ngakhale kuti ndinali kuwaphunzitsa, kudzuka m’mawa kwambiri ndi kuwaphunzitsa, palibe ngakhale mmodzi wa iwo amene anamvetsera kuti alandire mwambo.*+
24 Popeza ndaitana koma inu mukupitiriza kukana,+ ndatambasula dzanja langa koma palibe amene akumvetsera,+
12 Choncho ine ndidzakonzeratu zoti anthu inu mudzaphedwe ndi lupanga.+ Nonsenu mudzawerama kuti akupheni,+ popeza ndinakuitanani+ koma simunayankhe. Ndinalankhula koma simunamvere.+ Munapitiriza kuchita zinthu zoipa pamaso panga+ ndipo munasankha zinthu zimene sindisangalala nazo.”+
4 Ineyo ndidzasankha njira zowazunzira.+ Ndidzawabweretsera zinthu zimene amachita nazo mantha+ chifukwa ndinaitana koma palibe amene anayankha. Ndinalankhula koma palibe amene anamvera.+ Iwo anapitiriza kuchita zinthu zoipa pamaso panga ndipo anasankha zinthu zimene sindisangalala nazo.”+
13 Tsopano chifukwa chakuti mwapitiriza kuchita ntchito zimenezi,’ watero Yehova, ‘ndipo ndinali kukulankhulani nthawi zonse, kudzuka m’mamawa ndi kukulankhulani,+ koma inu osamva,+ kukuitanani koma inu osandiyankha,+
5 komanso kumvera mawu a atumiki anga aneneri amene ndikuwatumiza kwa inu, kudzuka m’mawa kwambiri ndi kuwatumiza, amene inu simunawamvere,+
33 Iwo anali kundifulatira, sanandiyang’ane.+ Ngakhale kuti ndinali kuwaphunzitsa, kudzuka m’mawa kwambiri ndi kuwaphunzitsa, palibe ngakhale mmodzi wa iwo amene anamvetsera kuti alandire mwambo.*+