Deuteronomo 28:53 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 53 Pamenepo udzadya chipatso cha mimba yako, mnofu wa ana ako aamuna ndi ana ako aakazi,+ amene Yehova Mulungu wako wakupatsa, chifukwa cha zovuta ndi nsautso zimene adani ako adzakupanikiza nazo. 2 Mafumu 25:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 M’mwezi wachinayi, pa tsiku la 9,+ njala+ inafika poipa kwambiri mumzindawo, ndipo anthu a m’dzikolo analibiretu chakudya.+ Yeremiya 38:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Inu mbuyanga mfumu, zimene anthu awa achitira mneneri Yeremiya ndi zoipa, chifukwa amuponya m’chitsime, ndipo afera momwemo+ chifukwa cha njala,+ pakuti mkate watheratu mumzindawu.”
53 Pamenepo udzadya chipatso cha mimba yako, mnofu wa ana ako aamuna ndi ana ako aakazi,+ amene Yehova Mulungu wako wakupatsa, chifukwa cha zovuta ndi nsautso zimene adani ako adzakupanikiza nazo.
3 M’mwezi wachinayi, pa tsiku la 9,+ njala+ inafika poipa kwambiri mumzindawo, ndipo anthu a m’dzikolo analibiretu chakudya.+
9 “Inu mbuyanga mfumu, zimene anthu awa achitira mneneri Yeremiya ndi zoipa, chifukwa amuponya m’chitsime, ndipo afera momwemo+ chifukwa cha njala,+ pakuti mkate watheratu mumzindawu.”