-
2 Mafumu 16:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Mfumuyo inachotsa chinthu chokhala ndi denga chogwiritsa ntchito pa sabata chimene anachimanga m’nyumba ya Yehova, ndipo inatsekanso khomo lakunja limene mfumu inali kulowera m’nyumbayo. Inachita zimenezi chifukwa choopa mfumu ya Asuri.
-