Yeremiya 6:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Iwe mwana wamkazi wa anthu anga, vala chiguduli*+ ndi kuvimvinizika m’phulusa.+ Lira ngati kuti ukulira maliro a mwana wamwamuna mmodzi yekhayo. Lira mowawidwa mtima+ chifukwa wofunkha adzatiukira modzidzimutsa.+ Yeremiya 10:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Hema wanga wafunkhidwa, ndipo zingwe zanga zonse zomangira hemayo aziduladula.+ Ana anga aamuna achoka ndi kundisiya ndipo kulibenso.+ Komanso palibe wotambasula kapena kudzutsa hema wanga.
26 Iwe mwana wamkazi wa anthu anga, vala chiguduli*+ ndi kuvimvinizika m’phulusa.+ Lira ngati kuti ukulira maliro a mwana wamwamuna mmodzi yekhayo. Lira mowawidwa mtima+ chifukwa wofunkha adzatiukira modzidzimutsa.+
20 Hema wanga wafunkhidwa, ndipo zingwe zanga zonse zomangira hemayo aziduladula.+ Ana anga aamuna achoka ndi kundisiya ndipo kulibenso.+ Komanso palibe wotambasula kapena kudzutsa hema wanga.