Maliro 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye akulira kwambiri usiku,+ ndipo misozi ikutsika pamasaya ake.+Pakati pa onse amene anali kumukonda, palibe amene akumutonthoza.+Anthu onse amene anali anzake amuchitira zachinyengo+ ndipo akhala adani ake.+ Maliro 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndikulirira zinthu zimenezi ngati mkazi.+ Maso anga ine! Maso anga akutuluka misozi.+Pakuti wonditonthoza, munthu woti anditsitsimule, ali kutali ndi ine.Ana anga asiyidwa+ popanda thandizo, pakuti mdani wanga wadzitukumula.+ Amosi 5:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Choncho Yehova, Mulungu wa makamu, Yehova wanena kuti, ‘Padzamveka kulira m’mabwalo onse a mizinda+ yanu ndipo m’misewu yanu yonse anthu azidzanena kuti: “Aa! Aa!” Pamenepo adzaitana mlimi kuti alire+ ndiponso anthu odziwa kulira maliro kuti alire mokweza.’+ Luka 7:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Atayandikira pachipata cha mzindawo, anakumana ndi anthu atanyamula maliro.+ Womwalirayo anali mwana wamwamuna yekhayo+ kwa mayi ake. Komanso mayi akewo anali mkazi wamasiye. Khamu lalikulu ndithu la anthu ochokera mumzindawo linali limodzi ndi mayiwo.
2 Iye akulira kwambiri usiku,+ ndipo misozi ikutsika pamasaya ake.+Pakati pa onse amene anali kumukonda, palibe amene akumutonthoza.+Anthu onse amene anali anzake amuchitira zachinyengo+ ndipo akhala adani ake.+
16 Ndikulirira zinthu zimenezi ngati mkazi.+ Maso anga ine! Maso anga akutuluka misozi.+Pakuti wonditonthoza, munthu woti anditsitsimule, ali kutali ndi ine.Ana anga asiyidwa+ popanda thandizo, pakuti mdani wanga wadzitukumula.+
16 “Choncho Yehova, Mulungu wa makamu, Yehova wanena kuti, ‘Padzamveka kulira m’mabwalo onse a mizinda+ yanu ndipo m’misewu yanu yonse anthu azidzanena kuti: “Aa! Aa!” Pamenepo adzaitana mlimi kuti alire+ ndiponso anthu odziwa kulira maliro kuti alire mokweza.’+
12 Atayandikira pachipata cha mzindawo, anakumana ndi anthu atanyamula maliro.+ Womwalirayo anali mwana wamwamuna yekhayo+ kwa mayi ake. Komanso mayi akewo anali mkazi wamasiye. Khamu lalikulu ndithu la anthu ochokera mumzindawo linali limodzi ndi mayiwo.