Yesaya 24:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Chotero pakatikati pa dzikolo, pakati pa anthu a mitundu ina, anthu anga adzakhala ngati zipatso zotsala mumtengo wa maolivi,+ ndiponso ngati zokunkha zotsala anthu akakolola mphesa.+ Yeremiya 49:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kodi okolola mphesa atabwera kwa iwe sadzasiyako zina zoti ena akunkhe? Ndipotu akuba atakubwerera usiku, adzangowononga zokhazo zimene akufuna.+
13 Chotero pakatikati pa dzikolo, pakati pa anthu a mitundu ina, anthu anga adzakhala ngati zipatso zotsala mumtengo wa maolivi,+ ndiponso ngati zokunkha zotsala anthu akakolola mphesa.+
9 Kodi okolola mphesa atabwera kwa iwe sadzasiyako zina zoti ena akunkhe? Ndipotu akuba atakubwerera usiku, adzangowononga zokhazo zimene akufuna.+