Ekisodo 24:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno Mose anapita kwa anthu ndi kuwafotokozera mawu onse a Yehova ndi zigamulo zake zonse.+ Pamenepo anthu onse anayankhira pamodzi kuti: “Mawu onse amene Yehova wanena tidzachita.”+
3 Ndiyeno Mose anapita kwa anthu ndi kuwafotokozera mawu onse a Yehova ndi zigamulo zake zonse.+ Pamenepo anthu onse anayankhira pamodzi kuti: “Mawu onse amene Yehova wanena tidzachita.”+