Levitiko 18:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Chotero muzisunga malamulo anga kuti musamachite iliyonse mwa miyambo yonyansa imene anthu akhala akuchita inu musanafike.+ Pamenepo mudzapewa kudzidetsa ndi miyamboyo. Ine ndine Yehova Mulungu wanu.’”
30 Chotero muzisunga malamulo anga kuti musamachite iliyonse mwa miyambo yonyansa imene anthu akhala akuchita inu musanafike.+ Pamenepo mudzapewa kudzidetsa ndi miyamboyo. Ine ndine Yehova Mulungu wanu.’”