Levitiko 18:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Choncho muzisunga malamulo anga popewa kuchita miyambo yonyansa iliyonse imene anthu akhala akuchita inu musanafike,+ kuti musadzidetse ndi miyamboyo. Ine ndine Yehova Mulungu wanu.’”
30 Choncho muzisunga malamulo anga popewa kuchita miyambo yonyansa iliyonse imene anthu akhala akuchita inu musanafike,+ kuti musadzidetse ndi miyamboyo. Ine ndine Yehova Mulungu wanu.’”