Salimo 106:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Choncho anasinthanitsa ulemerero wanga+Ndi chifaniziro cha ng’ombe yamphongo yodya udzu.+ Hoseya 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pamene iwo achuluka, m’pamenenso akundichimwira kwambiri.+ M’malo mondipatsa ulemu, akundinyoza.+ Aroma 1:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 ndipo anasandutsa ulemerero+ wa Mulungu amene sawonongeka kukhala ngati chifaniziro+ cha munthu, mbalame, zolengedwa za miyendo inayi ndi zokwawa,+ zonsezo zimene zimawonongeka.
23 ndipo anasandutsa ulemerero+ wa Mulungu amene sawonongeka kukhala ngati chifaniziro+ cha munthu, mbalame, zolengedwa za miyendo inayi ndi zokwawa,+ zonsezo zimene zimawonongeka.