Deuteronomo 32:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Anam’peza m’dziko lachipululu,+M’chipululu chopanda kanthu, molira zilombo zakutchire.+Pamenepo anayamba kum’zungulira,+ kum’samalira,+Kum’teteza monga mwana wa diso lake.+ Salimo 77:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mwatsogolera anthu anu ngati nkhosa,+Kudzera mwa Mose ndi Aroni.+ Salimo 78:54 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 54 Kenako anawalowetsa m’dziko lake lopatulika,+M’dera lamapiri ili limene dzanja lake lamanja linatenga.+ Salimo 136:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Yamikani amene anayendetsa anthu ake m’chipululu:+Pakuti kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+ Yesaya 63:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 amene anawawolotsa pamadzi amphamvu moti sanapunthwe, mofanana ndi hatchi m’chipululu?+
10 Anam’peza m’dziko lachipululu,+M’chipululu chopanda kanthu, molira zilombo zakutchire.+Pamenepo anayamba kum’zungulira,+ kum’samalira,+Kum’teteza monga mwana wa diso lake.+
54 Kenako anawalowetsa m’dziko lake lopatulika,+M’dera lamapiri ili limene dzanja lake lamanja linatenga.+
16 Yamikani amene anayendetsa anthu ake m’chipululu:+Pakuti kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+ Yesaya 63:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 amene anawawolotsa pamadzi amphamvu moti sanapunthwe, mofanana ndi hatchi m’chipululu?+