6 Iwo sananene kuti, ‘Ali kuti Yehova, amene anatitulutsa m’dziko la Iguputo,+ amene anatitsogolera m’chipululu,+ m’dera lam’chipululu lodzaza ndi mayenje, m’dziko lopanda madzi+ ndi la mdima wandiweyani,+ dziko limene simunadutse munthu aliyense komanso mmene simunali kukhala munthu aliyense?’