Yobu 34:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pakuti maso ake amayang’anitsitsa njira za munthu,+Ndipo amaona mayendedwe ake onse. Salimo 90:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Zolakwa zathu mwaziika patsogolo panu,+Ndipo machimo athu obisika* ali patsogolo pa nkhope yanu yowala.+ Miyambo 5:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pakuti njira za munthu zili pamaso pa Yehova,+ ndipo iye amaonetsetsa njira zake zonse.+ Miyambo 15:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Maso a Yehova ali paliponse.+ Amayang’ana anthu oipa ndi abwino omwe.+ Yeremiya 32:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Zolinga zanu ndi zazikulu+ ndipo zochita zanu ndi zambiri.+ Maso anu amaona njira zonse za ana a anthu+ kuti munthu aliyense mumuchitire zinthu mogwirizana ndi njira zake komanso zipatso za ntchito zake.+ Aheberi 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Palibe cholengedwa chimene Mulungu sangathe kuchiona.+ Chifukwa kwa iye zinthu zonse zili poonekera ndipo amatha kuziona bwinobwino. Ndipotu ife tikuyenera kudzayankha pa zochita zathu kwa Mulungu amene amaona zonseyo.+
8 Zolakwa zathu mwaziika patsogolo panu,+Ndipo machimo athu obisika* ali patsogolo pa nkhope yanu yowala.+
19 Zolinga zanu ndi zazikulu+ ndipo zochita zanu ndi zambiri.+ Maso anu amaona njira zonse za ana a anthu+ kuti munthu aliyense mumuchitire zinthu mogwirizana ndi njira zake komanso zipatso za ntchito zake.+
13 Palibe cholengedwa chimene Mulungu sangathe kuchiona.+ Chifukwa kwa iye zinthu zonse zili poonekera ndipo amatha kuziona bwinobwino. Ndipotu ife tikuyenera kudzayankha pa zochita zathu kwa Mulungu amene amaona zonseyo.+