Yesaya 40:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Taonani! Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, adzabwera ngati wamphamvu ndipo dzanja lake lizidzalamulira m’malo mwa iyeyo.+ Mphoto yake ili ndi iyeyo+ ndipo malipiro amene amapereka ali pamaso pake.+
10 Taonani! Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, adzabwera ngati wamphamvu ndipo dzanja lake lizidzalamulira m’malo mwa iyeyo.+ Mphoto yake ili ndi iyeyo+ ndipo malipiro amene amapereka ali pamaso pake.+