Yeremiya 33:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Yehova wa makamu wanena kuti, ‘M’dziko lino lopanda pake, lopanda anthu ndi lopanda ziweto+ ndi mizinda yake yonse, mudzakhala malo odyetserako ziweto kumene abusa adzalola ziweto zawo kugona pansi.’+ Ezekieli 25:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Ine ndidzatambasulira Edomu+ dzanja langa ndi kupha anthu ndi ziweto m’dzikolo.+ Ndidzalisandutsa bwinja kuyambira ku Temani+ mpaka ku Dedani.+ Iwo adzaphedwa ndi lupanga. Hoseya 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 N’chifukwa chake dzikoli lidzalira maliro+ ndipo aliyense wokhala mmenemo adzalefukiratu pamodzi ndi zilombo zakutchire ndi zolengedwa zouluka m’mlengalenga. Nsomba zam’nyanja nazonso zidzafa.+ Zefaniya 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Ndidzafafaniza anthu ndi nyama.+ Ndidzafafaniza zolengedwa zouluka m’mlengalenga, nsomba za m’nyanja,+ zokhumudwitsa pamodzi ndi anthu oipa,+ ndipo ndidzawononga anthu onse ndi kuwachotsa panthaka,”+ watero Yehova.
12 “Yehova wa makamu wanena kuti, ‘M’dziko lino lopanda pake, lopanda anthu ndi lopanda ziweto+ ndi mizinda yake yonse, mudzakhala malo odyetserako ziweto kumene abusa adzalola ziweto zawo kugona pansi.’+
13 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Ine ndidzatambasulira Edomu+ dzanja langa ndi kupha anthu ndi ziweto m’dzikolo.+ Ndidzalisandutsa bwinja kuyambira ku Temani+ mpaka ku Dedani.+ Iwo adzaphedwa ndi lupanga.
3 N’chifukwa chake dzikoli lidzalira maliro+ ndipo aliyense wokhala mmenemo adzalefukiratu pamodzi ndi zilombo zakutchire ndi zolengedwa zouluka m’mlengalenga. Nsomba zam’nyanja nazonso zidzafa.+
3 “Ndidzafafaniza anthu ndi nyama.+ Ndidzafafaniza zolengedwa zouluka m’mlengalenga, nsomba za m’nyanja,+ zokhumudwitsa pamodzi ndi anthu oipa,+ ndipo ndidzawononga anthu onse ndi kuwachotsa panthaka,”+ watero Yehova.