Yesaya 24:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Dzikolo likulira+ ndipo likuzimiririka. Nthaka ya dziko lapansi yafota ndipo yazimiririka. Anthu apamwamba a m’dzikolo afota.+ Yeremiya 4:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Pachifukwa chimenechi dziko lidzalira+ ndipo kumwamba kudzachita mdima.+ Izi zili choncho chifukwa ndanena, ndaganiza zimenezi mozama, sindinadziimbe mlandu ndipo sindisintha maganizo anga.+ Yoweli 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Munda wawonongedwa+ ndipo nthaka ikulira+ pakuti mbewu zawonongedwa. Vinyo watsopano wauma+ ndipo mafuta atha.+ Amosi 8:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pa chifukwa chimenechi dziko lidzagwedezeka,+ ndipo aliyense wokhala mmenemo adzalira.+ Dziko lonselo lidzasefukira ngati mtsinje wa Nailo ndi kuwinduka, ndipo kenako lidzaphwa ngati mtsinje wa Nailo wa ku Iguputo.’+
4 Dzikolo likulira+ ndipo likuzimiririka. Nthaka ya dziko lapansi yafota ndipo yazimiririka. Anthu apamwamba a m’dzikolo afota.+
28 Pachifukwa chimenechi dziko lidzalira+ ndipo kumwamba kudzachita mdima.+ Izi zili choncho chifukwa ndanena, ndaganiza zimenezi mozama, sindinadziimbe mlandu ndipo sindisintha maganizo anga.+
10 Munda wawonongedwa+ ndipo nthaka ikulira+ pakuti mbewu zawonongedwa. Vinyo watsopano wauma+ ndipo mafuta atha.+
8 Pa chifukwa chimenechi dziko lidzagwedezeka,+ ndipo aliyense wokhala mmenemo adzalira.+ Dziko lonselo lidzasefukira ngati mtsinje wa Nailo ndi kuwinduka, ndipo kenako lidzaphwa ngati mtsinje wa Nailo wa ku Iguputo.’+