Yeremiya 10:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma Yehova ndi Mulungu woonadi.+ Iye ndi Mulungu wamoyo+ ndipo ndi Mfumu mpaka kalekale.+ Dziko lapansi lidzagwedezeka ndi mkwiyo wake,+ ndipo palibe mitundu ya anthu imene idzalimbe pamene iye akuidzudzula.+ 1 Timoteyo 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kwa Mfumu yamuyaya,+ imene siifa,+ yosaoneka,+ yekhayo amene ali Mulungu,+ kwa iyeyo kupite ulemu ndi ulemerero mpaka muyaya.+ Ame. Chivumbulutso 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Ndinu woyenera, inu Yehova* Mulungu wathu wamphamvu,+ kulandira ulemerero+ ndi ulemu,+ chifukwa munalenga zinthu zonse,+ ndipo mwa kufuna kwanu,+ zinakhalapo ndipo zinalengedwa.”+
10 Koma Yehova ndi Mulungu woonadi.+ Iye ndi Mulungu wamoyo+ ndipo ndi Mfumu mpaka kalekale.+ Dziko lapansi lidzagwedezeka ndi mkwiyo wake,+ ndipo palibe mitundu ya anthu imene idzalimbe pamene iye akuidzudzula.+
17 Kwa Mfumu yamuyaya,+ imene siifa,+ yosaoneka,+ yekhayo amene ali Mulungu,+ kwa iyeyo kupite ulemu ndi ulemerero mpaka muyaya.+ Ame.
11 “Ndinu woyenera, inu Yehova* Mulungu wathu wamphamvu,+ kulandira ulemerero+ ndi ulemu,+ chifukwa munalenga zinthu zonse,+ ndipo mwa kufuna kwanu,+ zinakhalapo ndipo zinalengedwa.”+