Genesis 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako Mulungu anadalitsa tsiku la 7. Analipatula kuti likhale lopatulika, chifukwa kuyambira pa tsikuli, iye wakhala akupuma pa ntchito yake yonse yolenga ndi yopanga zimene anafuna.+
3 Kenako Mulungu anadalitsa tsiku la 7. Analipatula kuti likhale lopatulika, chifukwa kuyambira pa tsikuli, iye wakhala akupuma pa ntchito yake yonse yolenga ndi yopanga zimene anafuna.+