2 Anaikanso nduna zapamwamba zitatu zoyang’anira masatarapiwo, ndipo Danieli anali mmodzi wa ndunazo.+ Anaika nduna zimenezi kuti nthawi zonse masatarapiwo+ aziziuza chilichonse chimene chikuchitika, ndi cholinga chakuti zinthu za mfumu zisawonongeke.+