-
1 Samueli 2:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Yehova ndi Wopereka Umphawi+ ndi Wolemeretsa,+
Wotsitsa ndiponso Wokweza,+
-
Danieli 4:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Alonda+ ndi amene alamula zimenezi. Angelo oyera* ndi amene apempha zimenezi ndi cholinga chakuti anthu adziwe kuti Wam’mwambamwamba ndiye Wolamulira wa maufumu a anthu,+ ndiponso adziwe kuti iye akafuna kupereka ulamuliro kwa munthu aliyense, amamupatsa+ ndipo amaika ngakhale munthu wonyozeka kwambiri kuti azilamulira.”+
-
-
-