41 “Popeza munaona kuti mapazi ndi zala zakumiyendo zinali zadongo la woumba mbiya losakanizika ndi chitsulo,+ ufumuwo udzakhala wogawanika,+ koma udzakhala wolimba pa zinthu zina ngati chitsulo. Zimenezi zili choncho chifukwa munaona kuti chitsulocho chinali chosakanizika ndi dongo lonyowa.+