Numeri 25:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chotero Aisiraeli anayamba kupembedza nawo Baala wa ku Peori.+ Pamenepo, mkwiyo wa Yehova unawayakira.+ Deuteronomo 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Inu munaona ndi maso anu zimene Yehova anachita pa nkhani ya Baala wa ku Peori, kuti munthu aliyense amene anatsatira Baala wa ku Peori,+ Yehova Mulungu wanu anamuwononga ndi kum’chotsa pakati panu.+ Salimo 106:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Iwo anayamba kulambira Baala wa ku Peori,+Ndi kudya nsembe zoperekedwa ku zinthu zakufa.+
3 Chotero Aisiraeli anayamba kupembedza nawo Baala wa ku Peori.+ Pamenepo, mkwiyo wa Yehova unawayakira.+
3 “Inu munaona ndi maso anu zimene Yehova anachita pa nkhani ya Baala wa ku Peori, kuti munthu aliyense amene anatsatira Baala wa ku Peori,+ Yehova Mulungu wanu anamuwononga ndi kum’chotsa pakati panu.+