Salimo 50:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pa tsiku la nsautso undiitane.+Ine ndidzakulanditsa, ndipo iwe udzandilemekeza.”+ Salimo 91:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Adzandiitana ndipo ndidzamuyankha.+Ndidzakhala naye m’nthawi ya masautso.+Ndidzamupulumutsa ndi kumupatsa ulemerero.+ Mika 7:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma ine ndidzadikirira Yehova.+ Ndidzayembekezera moleza mtima Mulungu wa chipulumutso changa.+ Mulungu wanga adzandimvera.+ Habakuku 3:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ine ndidzakondwerabe mwa Yehova+ ndipo ndidzasangalala mwa Mulungu wachipulumutso changa.+ Afilipi 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Musamade nkhawa ndi kanthu kalikonse,+ koma pa chilichonse, mwa pemphero ndi pembedzero,+ pamodzi ndi chiyamiko, zopempha zanu zidziwike kwa Mulungu.+
15 Adzandiitana ndipo ndidzamuyankha.+Ndidzakhala naye m’nthawi ya masautso.+Ndidzamupulumutsa ndi kumupatsa ulemerero.+
7 Koma ine ndidzadikirira Yehova.+ Ndidzayembekezera moleza mtima Mulungu wa chipulumutso changa.+ Mulungu wanga adzandimvera.+
6 Musamade nkhawa ndi kanthu kalikonse,+ koma pa chilichonse, mwa pemphero ndi pembedzero,+ pamodzi ndi chiyamiko, zopempha zanu zidziwike kwa Mulungu.+