Yeremiya 4:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Pachifukwa chimenechi dziko lidzalira+ ndipo kumwamba kudzachita mdima.+ Izi zili choncho chifukwa ndanena, ndaganiza zimenezi mozama, sindinadziimbe mlandu ndipo sindisintha maganizo anga.+ Yoweli 2:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Dzuwa lidzasanduka mdima,+ ndipo mwezi udzasanduka magazi.+ Zimenezi zidzachitika tsiku lalikulu ndi lochititsa mantha la Yehova lisanafike.+ Mateyu 24:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 “Chisautso cha masiku amenewo chikadzangotha, dzuwa lidzachita mdima+ ndipo mwezi+ sudzapereka kuwala kwake. Nyenyezi zidzagwa kuchokera kumwamba, ndipo mphamvu za kumwamba zidzagwedezeka.+ Luka 21:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 “Komanso, padzakhala zizindikiro padzuwa,+ mwezi ndi nyenyezi. Padziko lapansi anthu a mitundu ina adzazunzika, ndipo adzathedwa nzeru chifukwa cha mkokomo wa nyanja+ ndi kuwinduka kwake.+ Machitidwe 2:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Dzuwa+ lidzasanduka mdima, ndipo mwezi udzasanduka magazi. Zimenezi zidzachitika tsiku lalikulu ndi laulemerero la Yehova* lisanafike.+ Chivumbulutso 9:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pamene inatsegula dzenje lolowera kuphompholo, utsi+ ngati wa m’ng’anjo yaikulu+ unatuluka m’dzenjemo, ndipo dzuwa ndi mpweya zinada+ ndi utsi wa m’dzenjewo.
28 Pachifukwa chimenechi dziko lidzalira+ ndipo kumwamba kudzachita mdima.+ Izi zili choncho chifukwa ndanena, ndaganiza zimenezi mozama, sindinadziimbe mlandu ndipo sindisintha maganizo anga.+
31 Dzuwa lidzasanduka mdima,+ ndipo mwezi udzasanduka magazi.+ Zimenezi zidzachitika tsiku lalikulu ndi lochititsa mantha la Yehova lisanafike.+
29 “Chisautso cha masiku amenewo chikadzangotha, dzuwa lidzachita mdima+ ndipo mwezi+ sudzapereka kuwala kwake. Nyenyezi zidzagwa kuchokera kumwamba, ndipo mphamvu za kumwamba zidzagwedezeka.+
25 “Komanso, padzakhala zizindikiro padzuwa,+ mwezi ndi nyenyezi. Padziko lapansi anthu a mitundu ina adzazunzika, ndipo adzathedwa nzeru chifukwa cha mkokomo wa nyanja+ ndi kuwinduka kwake.+
20 Dzuwa+ lidzasanduka mdima, ndipo mwezi udzasanduka magazi. Zimenezi zidzachitika tsiku lalikulu ndi laulemerero la Yehova* lisanafike.+
2 Pamene inatsegula dzenje lolowera kuphompholo, utsi+ ngati wa m’ng’anjo yaikulu+ unatuluka m’dzenjemo, ndipo dzuwa ndi mpweya zinada+ ndi utsi wa m’dzenjewo.