Deuteronomo 28:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Udzalimadi ndi kubzala mitengo ya mpesa, koma sudzakolola mphesa zake ndi kumwa vinyo,+ chifukwa mbozi zidzadya mpesawo.+ Yesaya 32:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pomatha chaka ndi masiku angapo, anthu osasamalanu mudzatekeseka,+ chifukwa ngakhale nyengo yokolola mphesa itatha, sipadzakhala mphesa zilizonse zimene zasonkhanitsidwa.+
39 Udzalimadi ndi kubzala mitengo ya mpesa, koma sudzakolola mphesa zake ndi kumwa vinyo,+ chifukwa mbozi zidzadya mpesawo.+
10 Pomatha chaka ndi masiku angapo, anthu osasamalanu mudzatekeseka,+ chifukwa ngakhale nyengo yokolola mphesa itatha, sipadzakhala mphesa zilizonse zimene zasonkhanitsidwa.+