Yeremiya 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pamenepo Yehova anandiuza kuti: “Usanene kuti, ‘Ndine mwana.’ Koma upite kwa anthu onse amene ndidzakutumako. Ndipo ukanene zonse zimene ndidzakulamula kuti ukanene.+ Ezekieli 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iye anandiuza kuti: “Iwe mwana wa munthu, ndikukutumiza kwa ana a Isiraeli,+ kwa mitundu yopanduka imene yandipandukira.+ Iwo ndi makolo awo akhala akuphwanya malamulo anga mpaka lero.+ 2 Petulo 1:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Chifukwa ulosi sunayambe wanenedwapo mwa kufuna kwa munthu,+ koma anthu analankhula mawu ochokera kwa Mulungu+ motsogoleredwa ndi mzimu woyera.+
7 Pamenepo Yehova anandiuza kuti: “Usanene kuti, ‘Ndine mwana.’ Koma upite kwa anthu onse amene ndidzakutumako. Ndipo ukanene zonse zimene ndidzakulamula kuti ukanene.+
3 Iye anandiuza kuti: “Iwe mwana wa munthu, ndikukutumiza kwa ana a Isiraeli,+ kwa mitundu yopanduka imene yandipandukira.+ Iwo ndi makolo awo akhala akuphwanya malamulo anga mpaka lero.+
21 Chifukwa ulosi sunayambe wanenedwapo mwa kufuna kwa munthu,+ koma anthu analankhula mawu ochokera kwa Mulungu+ motsogoleredwa ndi mzimu woyera.+