Miyambo 1:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Pa nthawi imeneyo azidzangondiitana koma sindidzayankha.+ Adzakhalira kundifunafuna koma sadzandipeza,+ Yesaya 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mukatambasula manja anu,+ ndimakubisirani maso anga.+ Ngakhale mupereke mapemphero ambiri,+ ine sindimvetsera.+ Manja anu adzaza magazi amene mwakhetsa.+ Yohane 9:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Tikudziwa kuti Mulungu samvetsera ochimwa,+ koma ngati munthu ali woopa Mulungu ndipo amachita chifuniro chake, ameneyo amamumvetsera.+
28 Pa nthawi imeneyo azidzangondiitana koma sindidzayankha.+ Adzakhalira kundifunafuna koma sadzandipeza,+
15 Mukatambasula manja anu,+ ndimakubisirani maso anga.+ Ngakhale mupereke mapemphero ambiri,+ ine sindimvetsera.+ Manja anu adzaza magazi amene mwakhetsa.+
31 Tikudziwa kuti Mulungu samvetsera ochimwa,+ koma ngati munthu ali woopa Mulungu ndipo amachita chifuniro chake, ameneyo amamumvetsera.+