Miyambo 21:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Aliyense wotseka khutu lake kuti asamve kudandaula kwa munthu wonyozeka,+ nayenso adzaitana koma sadzayankhidwa.+ Yesaya 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mukatambasula manja anu,+ ndimakubisirani maso anga.+ Ngakhale mupereke mapemphero ambiri,+ ine sindimvetsera.+ Manja anu adzaza magazi amene mwakhetsa.+ Maliro 3:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Mwadzitchinga ndi mtambo waukulu+ kuti pemphero lisadutse ndi kufika kwa inu.+
13 Aliyense wotseka khutu lake kuti asamve kudandaula kwa munthu wonyozeka,+ nayenso adzaitana koma sadzayankhidwa.+
15 Mukatambasula manja anu,+ ndimakubisirani maso anga.+ Ngakhale mupereke mapemphero ambiri,+ ine sindimvetsera.+ Manja anu adzaza magazi amene mwakhetsa.+