Salimo 69:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pakuti iwo amalondalonda munthu amene inu mwamulanga,+Ndipo amakamba za ululu wa anthu amene inu mwawalasa. Salimo 137:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Inu Yehova, kumbukirani+ zimene ana a Edomu+ ananena pa tsiku limene Yerusalemu anawonongedwa,+Iwo anati: “Fafanizani mzindawo! Ufafanizeni mpaka pamaziko ake!”+ Yesaya 47:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ine ndinakwiyira anthu anga.+ Ndinanyoza cholowa changa+ ndipo ndinawapereka m’manja mwako.+ Iwe sunawachitire chifundo.+ Munthu wokalamba unamusenzetsa goli lolemera kwambiri.+ Yeremiya 51:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Mkazi wokhala mu Ziyoni adzanena kuti, ‘Chiwawa chimene achitira ine ndi thupi langa chigwerenso Babulo.’+ Yerusalemu adzanena kuti, ‘Magazi anga akhale pa anthu okhala m’dziko la Kasidi.’”+
26 Pakuti iwo amalondalonda munthu amene inu mwamulanga,+Ndipo amakamba za ululu wa anthu amene inu mwawalasa.
7 Inu Yehova, kumbukirani+ zimene ana a Edomu+ ananena pa tsiku limene Yerusalemu anawonongedwa,+Iwo anati: “Fafanizani mzindawo! Ufafanizeni mpaka pamaziko ake!”+
6 Ine ndinakwiyira anthu anga.+ Ndinanyoza cholowa changa+ ndipo ndinawapereka m’manja mwako.+ Iwe sunawachitire chifundo.+ Munthu wokalamba unamusenzetsa goli lolemera kwambiri.+
35 Mkazi wokhala mu Ziyoni adzanena kuti, ‘Chiwawa chimene achitira ine ndi thupi langa chigwerenso Babulo.’+ Yerusalemu adzanena kuti, ‘Magazi anga akhale pa anthu okhala m’dziko la Kasidi.’”+