Machitidwe 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iye anawayankha kuti: “Si kwa inu kudziwa nthawi kapena nyengo+ zimene Atate waziika pansi pa ulamuliro wake.+ 1 Atesalonika 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma tsopano za nthawi ndi nyengo+ abale, simukufunika kukulemberani kanthu.
7 Iye anawayankha kuti: “Si kwa inu kudziwa nthawi kapena nyengo+ zimene Atate waziika pansi pa ulamuliro wake.+