Danieli 2:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Iye amasintha nthawi ndi nyengo,+ amachotsa mafumu ndi kuika mafumu,+ amapereka nzeru kwa anthu anzeru ndiponso amachititsa kuti anthu ozindikira adziwe zinthu.+ Danieli 7:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Idzalankhula mawu otsutsana ndi Wam’mwambamwamba+ ndipo idzazunza mosalekeza oyera a Wamkulukulu.+ Idzafuna kusintha nthawi+ ndiponso lamulo+ ndipo oyerawo adzaperekedwa m’manja mwake kwa nthawi imodzi, nthawi ziwiri, ndi hafu ya nthawi.+ Luka 21:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Anthu adzaphedwa ndi lupanga ndiponso kutengedwa ukapolo kupita nawo ku mitundu ina yonse.+ Anthu a mitundu ina adzapondaponda Yerusalemu, kufikira nthawi zoikidwiratu+ za anthu a mitundu inawo zitakwanira.
21 Iye amasintha nthawi ndi nyengo,+ amachotsa mafumu ndi kuika mafumu,+ amapereka nzeru kwa anthu anzeru ndiponso amachititsa kuti anthu ozindikira adziwe zinthu.+
25 Idzalankhula mawu otsutsana ndi Wam’mwambamwamba+ ndipo idzazunza mosalekeza oyera a Wamkulukulu.+ Idzafuna kusintha nthawi+ ndiponso lamulo+ ndipo oyerawo adzaperekedwa m’manja mwake kwa nthawi imodzi, nthawi ziwiri, ndi hafu ya nthawi.+
24 Anthu adzaphedwa ndi lupanga ndiponso kutengedwa ukapolo kupita nawo ku mitundu ina yonse.+ Anthu a mitundu ina adzapondaponda Yerusalemu, kufikira nthawi zoikidwiratu+ za anthu a mitundu inawo zitakwanira.