Luka 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho Mdyerekeziyo atamaliza mayesero onsewo, anamusiya kufikira nthawi ina yabwino.+ Yakobo 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Choncho gonjerani+ Mulungu, koma tsutsani Mdyerekezi+ ndipo adzakuthawani.+