Mateyu 26:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Yesu anamuuza kuti: “Ndithu ndikukuuza iwe, Usiku womwe uno tambala asanalire, undikana katatu.”+ Maliko 14:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Pamenepo Yesu anamuuza kuti: “Ndithu ndikukuuza, iweyo lero, usiku womwe uno, tambala asanalire kawiri, undikana katatu.”+ Yohane 13:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Yesu anayankha kuti: “Kodi udzapereka moyo wako chifukwa cha ine? Ndithudi ndikukuuza iwe, Tambala asanalire undikana katatu.”+
30 Pamenepo Yesu anamuuza kuti: “Ndithu ndikukuuza, iweyo lero, usiku womwe uno, tambala asanalire kawiri, undikana katatu.”+
38 Yesu anayankha kuti: “Kodi udzapereka moyo wako chifukwa cha ine? Ndithudi ndikukuuza iwe, Tambala asanalire undikana katatu.”+