Maliko 15:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Choncho Pilato anamufunsa kuti: “Kodi ndiwe mfumu+ ya Ayuda?” Iye anayankha kuti: “Mukunena nokha.”+ Luka 23:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tsopano Pilato anamufunsa funso kuti: “Kodi ndiwe mfumu ya Ayuda?” Pomuyankha iye anati: “Mukunena nokha.”+ Yohane 18:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Choncho Pilato analowanso m’nyumba ya bwanamkubwa n’kuitana Yesu ndi kumufunsa kuti: “Kodi ndiwe mfumu ya Ayuda?”+
2 Choncho Pilato anamufunsa kuti: “Kodi ndiwe mfumu+ ya Ayuda?” Iye anayankha kuti: “Mukunena nokha.”+
3 Tsopano Pilato anamufunsa funso kuti: “Kodi ndiwe mfumu ya Ayuda?” Pomuyankha iye anati: “Mukunena nokha.”+
33 Choncho Pilato analowanso m’nyumba ya bwanamkubwa n’kuitana Yesu ndi kumufunsa kuti: “Kodi ndiwe mfumu ya Ayuda?”+