Maliko 15:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Ndiyeno Yesu anafuula mokweza mawu, ndipo anatsirizika.+ Luka 23:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Pamenepo Yesu anafuula mokweza mawu kuti: “Atate, ndikuikiza mzimu*+ wanga m’manja mwanu.” Atanena zimenezi anatsirizika.+ Yohane 19:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Atalandira vinyo wowawasayo, Yesu anati: “Ndakwaniritsa chifuniro chanu!”+ ndipo anaweramitsa mutu, ndi kupereka mzimu wake.+
46 Pamenepo Yesu anafuula mokweza mawu kuti: “Atate, ndikuikiza mzimu*+ wanga m’manja mwanu.” Atanena zimenezi anatsirizika.+
30 Atalandira vinyo wowawasayo, Yesu anati: “Ndakwaniritsa chifuniro chanu!”+ ndipo anaweramitsa mutu, ndi kupereka mzimu wake.+