Maliko 15:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Ndiyeno Yosefe anagula nsalu yabwino kwambiri ndi kumutsitsa. Atatero anamukulunga ndi nsalu yabwino kwambiri ija ndi kumuika+ m’manda+ amene anawasema m’thanthwe. Anagubuduza chimwala ndi kutseka pakhomo la manda achikumbutsowo.+ Luka 23:53 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 53 Choncho anautsitsa+ ndi kuukulunga munsalu yabwino kwambiri, kenako anakauika m’manda+ ogobedwa muthanthwe, mmene anali asanaikemo munthu chikhalire.+ Yohane 19:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Choncho iwo anatenga mtembo wa Yesu n’kuukulunga ndi nsalu zamaliro zonunkhira,+ malinga ndi mwambo umene Ayuda anali kutsatira poika maliro.
46 Ndiyeno Yosefe anagula nsalu yabwino kwambiri ndi kumutsitsa. Atatero anamukulunga ndi nsalu yabwino kwambiri ija ndi kumuika+ m’manda+ amene anawasema m’thanthwe. Anagubuduza chimwala ndi kutseka pakhomo la manda achikumbutsowo.+
53 Choncho anautsitsa+ ndi kuukulunga munsalu yabwino kwambiri, kenako anakauika m’manda+ ogobedwa muthanthwe, mmene anali asanaikemo munthu chikhalire.+
40 Choncho iwo anatenga mtembo wa Yesu n’kuukulunga ndi nsalu zamaliro zonunkhira,+ malinga ndi mwambo umene Ayuda anali kutsatira poika maliro.