Maliko 15:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Komanso, iwo anasenzetsa mtengo wake wozunzikirapo* munthu wongodutsa, dzina lake Simoni wa ku Kurene, amene anali kuchokera kudera la kumidzi, bambo wa Alekizanda ndi Rufu.+
21 Komanso, iwo anasenzetsa mtengo wake wozunzikirapo* munthu wongodutsa, dzina lake Simoni wa ku Kurene, amene anali kuchokera kudera la kumidzi, bambo wa Alekizanda ndi Rufu.+