Maliko 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Tsopano atangotsika m’ngalawa, anakumana ndi munthu wogwidwa ndi mzimu wonyansa akuchokera m’manda achikumbutso.+ Luka 8:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Koma atangotsika n’kufika kumtunda, anakumana ndi munthu wina waziwanda wochokera mumzindawo. Kwa nthawi yaitali ndithu, munthuyo anali kungokhala osavala, komanso sanali kukhala kunyumba, koma kumanda.+
2 Tsopano atangotsika m’ngalawa, anakumana ndi munthu wogwidwa ndi mzimu wonyansa akuchokera m’manda achikumbutso.+
27 Koma atangotsika n’kufika kumtunda, anakumana ndi munthu wina waziwanda wochokera mumzindawo. Kwa nthawi yaitali ndithu, munthuyo anali kungokhala osavala, komanso sanali kukhala kunyumba, koma kumanda.+